所属专辑:MTMTMK
歌手: The Very Best
时长: 04:13
Yoshua Alikuti - The Very Best[00:00:00]
Ana a mulungu[00:00:16]
Aisiraeli azunzika m'chipululu[00:00:18]
Bambo Mose musatayilire[00:00:25]
Namalenga ati mulamulire[00:00:29]
Lero mwataya chipangano[00:00:33]
Kuyamba kupembedza makavalo[00:00:37]
Alikuti yoswayo[00:00:42]
Adzabwera liti[00:00:46]
Tifuna chipulumutso[00:00:48]
Wanyoza mtundu wanga[00:00:52]
Iwe walakwa[00:00:56]
Walakwa[00:00:57]
Waphetsa mtundu wanga[00:01:01]
Ndati walakwa[00:01:05]
Ndati walakwa[00:01:06]
Alikuti yosuayo[00:01:08]
Adzabwera liti[00:01:12]
Tifuna chipulumutso[00:01:14]
Sitifuna mose wina[00:01:17]
Wankhambakamwa[00:01:21]
Wodzatisocheretsa[00:01:22]
Alikuti yosuayo[00:01:25]
Adzabwera liti[00:01:30]
Tifuna chipulumutso[00:01:31]
Sitifuna mose wina[00:01:34]
Wankhambakamwa[00:01:38]
Wodzatisocheretsa[00:01:40]
Ulendo wochokera kwa iguputo[00:01:44]
Unali wautali[00:01:49]
Munatiwolotsa yolodani bwinobwino[00:01:52]
Nanga lero bwanji[00:01:57]
Kabwino konse upange ulalike utakwera chulu[00:02:01]
Namalenga sakondwa nazo[00:02:10]
Mphoto yako[00:02:13]
Udzalandiliratu[00:02:15]
Wanyoza mtundu wanga[00:02:18]
Iwe walakwa walakwa[00:02:23]
Waphetsa mtundu wanga[00:02:27]
Ndati walakwa[00:02:31]
Ndati walakwa[00:02:32]
Alikuti yosuayo[00:02:35]
Adzabwera liti[00:02:39]
Tifuna chipulumutso[00:02:40]
Sitifuna mose wina[00:02:43]
Wankhambakamwa[00:02:47]
Wodzatisocheretsa[00:02:49]
Alikuti yosuayo[00:02:52]
Adzabwera liti[00:02:56]
Tifuna chipulumutso[00:02:58]
Sitifuna mose wina[00:03:01]
Wankhambakamwa[00:03:04]
Wodzatisocheretsa[00:03:06]
Alikuti yosuayo[00:03:09]
Adzabwera liti[00:03:13]
Tifuna chipulumutso[00:03:15]
Sitifuna mose wina[00:03:18]
Wankhambakamwa[00:03:22]
Wodzatisocheretsa[00:03:24]